-1
points
Kodi matenda a chimanga amayamba bwanji

Maize (corn)    Nkhotakota,Malawi

Nanga ungatete bwanji chimanga kuti chiasakhuzidwe ndi vutolo


Posted by: MATIAS NKHATA (1 point) MATIAS NKHATA
Posted: July 9, 2024




Answers

0
points
Pogwilitsa ntchito njira zina za makolo,kumbali ya mankhwala


Posted by: John Kamkwamba (2 points) John Kamkwamba
Posted: July 23, 2024




0
points
pogwiritsa ntchito mbewu zosavomerezeka ndi ma company opanga mbewu, mbewu zoterezi sizichedwa kugwidwa matenda


Posted by: precious kandoje (2 points) precious kandoje
Posted: September 5, 2024




You need to log in if you'd like to add an answer or comment.
Heart Heart icon